2 Mbiri 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso Manase anakonza guwa lansembe la Yehova+ nʼkuyamba kuperekapo nsembe zamgwirizano+ ndi nsembe zoyamikira,+ ndipo anauza Ayuda kuti azitumikira Yehova Mulungu wa Isiraeli.
16 Komanso Manase anakonza guwa lansembe la Yehova+ nʼkuyamba kuperekapo nsembe zamgwirizano+ ndi nsembe zoyamikira,+ ndipo anauza Ayuda kuti azitumikira Yehova Mulungu wa Isiraeli.