-
2 Mbiri 33:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Nkhani zokhudza pemphero lake,+ zokhudza mmene Mulungu anamvera pemphero lake lochonderera, machimo ake onse komanso kusakhulupirika kwake+ zinalembedwa mʼmawu a amasomphenya ake. Munalembedwanso nkhani zokhudza kumene iye anamangako malo okwezeka nʼkuikako mizati yopatulika*+ ndi zifaniziro zogoba iye asanadzichepetse.
-