2 Mbiri 33:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amoni+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 22 ndipo analamulira zaka ziwiri ku Yerusalemu.+