2 Mbiri 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita nthawi, atumiki ake anamukonzera chiwembu+ ndipo anamuphera mʼnyumba mwake.