2 Mbiri 33:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma anthu amʼdzikolo anapha anthu onse amene anachitira chiwembu Mfumu Amoni.+ Kenako anthuwo anaika mwana wake Yosiya+ kuti akhale mfumu mʼmalo mwake.
25 Koma anthu amʼdzikolo anapha anthu onse amene anachitira chiwembu Mfumu Amoni.+ Kenako anthuwo anaika mwana wake Yosiya+ kuti akhale mfumu mʼmalo mwake.