2 Mbiri 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yosiya anagwetsamo maguwa ansembe. Anaphwanya mizati yopatulika* ndi zifaniziro zogoba+ nʼkuziperapera ndipo anagumula zofukizira zonse mʼdziko lonse la Isiraeli.+ Atatero anabwerera ku Yerusalemu.
7 Yosiya anagwetsamo maguwa ansembe. Anaphwanya mizati yopatulika* ndi zifaniziro zogoba+ nʼkuziperapera ndipo anagumula zofukizira zonse mʼdziko lonse la Isiraeli.+ Atatero anabwerera ku Yerusalemu.