2 Mbiri 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼchaka cha 18 cha ulamuliro wake, atayeretsa dzikolo ndiponso kachisi,* iye anatuma Safani+ mwana wa Azaliya, Maaseya mkulu wa mzinda ndi Yowa mwana wa Yowahazi wolemba zochitika, kuti akakonze nyumba ya Yehova Mulungu wake.+
8 Mʼchaka cha 18 cha ulamuliro wake, atayeretsa dzikolo ndiponso kachisi,* iye anatuma Safani+ mwana wa Azaliya, Maaseya mkulu wa mzinda ndi Yowa mwana wa Yowahazi wolemba zochitika, kuti akakonze nyumba ya Yehova Mulungu wake.+