-
2 Mbiri 34:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako ndalamazo anazipereka kwa anthu amene anasankhidwa kuti aziyangʼanira ntchito panyumba ya Yehova. Ndiyeno anthu amene ankagwira ntchito panyumba ya Yehova anagwiritsa ntchito ndalamazo pokonza nyumbayo.
-