2 Mbiri 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Safani mlembi anauza mfumuyo kuti: “Wansembe Hilikiya wandipatsa buku linalake.”+ Ndiyeno Safani anayamba kuwerengera mfumu bukulo.+
18 Kenako Safani mlembi anauza mfumuyo kuti: “Wansembe Hilikiya wandipatsa buku linalake.”+ Ndiyeno Safani anayamba kuwerengera mfumu bukulo.+