2 Mbiri 34:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 chifukwa chakuti mtima wako unali womvera* ndipo unadzichepetsa pamaso pa Mulungu utamva mawu ake okhudza malo ano ndi anthu ake komanso unadzichepetsa pamaso panga nʼkungʼamba zovala zako ndi kulira pamaso panga, inenso ndamva,+ watero Yehova.
27 chifukwa chakuti mtima wako unali womvera* ndipo unadzichepetsa pamaso pa Mulungu utamva mawu ake okhudza malo ano ndi anthu ake komanso unadzichepetsa pamaso panga nʼkungʼamba zovala zako ndi kulira pamaso panga, inenso ndamva,+ watero Yehova.