30 Zitatero, mfumuyo inapita kunyumba ya Yehova limodzi ndi amuna onse a ku Yuda, anthu okhala ku Yerusalemu, ansembe, Alevi ndi anthu onse, ana ndi akulu omwe. Mfumuyo inawawerengera mawu onse amʼbuku la pangano limene linapezeka mʼnyumba ya Yehova.+