2 Mbiri 34:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kenako Yosiya anachotsa zonyansa* zonse mʼmadera onse a Aisiraeli+ ndipo anachititsa kuti anthu onse a ku Isiraeli azitumikira Yehova Mulungu wawo. Pa nthawi yonse ya moyo wa Yosiya, iwo sanasiye kutsatira Yehova Mulungu wa makolo awo. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:33 Nsanja ya Olonda,12/1/2005, tsa. 21
33 Kenako Yosiya anachotsa zonyansa* zonse mʼmadera onse a Aisiraeli+ ndipo anachititsa kuti anthu onse a ku Isiraeli azitumikira Yehova Mulungu wawo. Pa nthawi yonse ya moyo wa Yosiya, iwo sanasiye kutsatira Yehova Mulungu wa makolo awo.