2 Mbiri 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Konzekani mogwirizana ndi nyumba za makolo anu komanso magulu anu, potsatira zimene analemba Davide+ mfumu ya Isiraeli ndiponso mwana wake Solomo.+
4 Konzekani mogwirizana ndi nyumba za makolo anu komanso magulu anu, potsatira zimene analemba Davide+ mfumu ya Isiraeli ndiponso mwana wake Solomo.+