2 Mbiri 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yosiya anapereka ziweto zokwana 30,000 kwa anthu kuti zikhale nsembe ya Pasika ya anthu onse amene analipo. Anapereka ana a nkhosa amphongo ndi ana a mbuzi amphongo ndiponso ngʼombe 3,000. Zonsezi zinachokera pa katundu wa mfumu.+
7 Yosiya anapereka ziweto zokwana 30,000 kwa anthu kuti zikhale nsembe ya Pasika ya anthu onse amene analipo. Anapereka ana a nkhosa amphongo ndi ana a mbuzi amphongo ndiponso ngʼombe 3,000. Zonsezi zinachokera pa katundu wa mfumu.+