2 Mbiri 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yosiya anadzisintha+ nʼkupitabe kukamenyana naye. Iye sanamvere mawu a Neko omwe anali ochokera kwa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye mʼchigwa cha Megido.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2017, tsa. 27
22 Koma Yosiya anadzisintha+ nʼkupitabe kukamenyana naye. Iye sanamvere mawu a Neko omwe anali ochokera kwa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye mʼchigwa cha Megido.+