2 Mbiri 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mfumu ya Iguputo inamuchotsa pa udindo wake ku Yerusalemu, nʼkulamula anthu amʼdzikolo kuti aipatse matalente* 100 a siliva ndi talente imodzi ya golide.+
3 Koma mfumu ya Iguputo inamuchotsa pa udindo wake ku Yerusalemu, nʼkulamula anthu amʼdzikolo kuti aipatse matalente* 100 a siliva ndi talente imodzi ya golide.+