2 Mbiri 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako, mfumu ya Iguputo inaika Eliyakimu, mʼbale wake wa Yehoahazi, kukhala mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu ndipo inamusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Koma Neko+ anatenga Yehoahazi, mʼbale wake wa Eliyakimu, nʼkupita naye ku Iguputo.+
4 Kenako, mfumu ya Iguputo inaika Eliyakimu, mʼbale wake wa Yehoahazi, kukhala mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu ndipo inamusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Koma Neko+ anatenga Yehoahazi, mʼbale wake wa Eliyakimu, nʼkupita naye ku Iguputo.+