2 Mbiri 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zedekiya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 21 ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+