2 Mbiri 36:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zimenezi zinachitika pokwaniritsa mawu a Yehova amene ananena kudzera mwa Yeremiya,+ mpaka pamene dzikolo linalipira masabata ake.+ Masiku onse amene dzikolo linali bwinja linkasunga sabata mpaka zinakwana zaka 70.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:21 Nsanja ya Olonda,11/15/2006, tsa. 32
21 Zimenezi zinachitika pokwaniritsa mawu a Yehova amene ananena kudzera mwa Yeremiya,+ mpaka pamene dzikolo linalipira masabata ake.+ Masiku onse amene dzikolo linali bwinja linkasunga sabata mpaka zinakwana zaka 70.+