Ezara 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mʼchaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya, pokwaniritsa mawu a Yehova amene analankhula kudzera mwa Yeremiya,+ Yehova analimbikitsa Koresi mfumu ya Perisiya kuti alengeze mu ufumu wake wonse, zomwenso iye analemba mʼmakalata,+ kuti: Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, tsa. 229/1/1987, tsa. 271/15/1986, tsa. 7
1 Mʼchaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya, pokwaniritsa mawu a Yehova amene analankhula kudzera mwa Yeremiya,+ Yehova analimbikitsa Koresi mfumu ya Perisiya kuti alengeze mu ufumu wake wonse, zomwenso iye analemba mʼmakalata,+ kuti: