-
Ezara 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno atsogoleri a mabanja a fuko la Yuda, la Benjamini, ansembe, Alevi ndi aliyense amene Mulungu woona analimbikitsa mtima wake, anakonzeka kuti apite kukamanganso nyumba ya Yehova, yomwe inali ku Yerusalemu.
-