Ezara 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu onse oyandikana nawo anawathandiza* powapatsa ziwiya zasiliva, zagolide, ziweto, zinthu zina zamtengo wapatali komanso katundu wosiyanasiyana, kuwonjezera pa zonse zimene zinaperekedwa mwaufulu.
6 Anthu onse oyandikana nawo anawathandiza* powapatsa ziwiya zasiliva, zagolide, ziweto, zinthu zina zamtengo wapatali komanso katundu wosiyanasiyana, kuwonjezera pa zonse zimene zinaperekedwa mwaufulu.