Ezara 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati kuti abweretse ziwiyazo nʼkuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda. Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Nsanja ya Olonda,1/15/1986, tsa. 8
8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati kuti abweretse ziwiyazo nʼkuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda.