Ezara 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amenewa anabwera pamodzi ndi Zerubabele,+ Yesuwa,*+ Nehemiya, Seraya, Reelaya, Moredikayi, Bilisani, Misipara, Bigivai, Rehumu ndi Bana. Chiwerengero cha amuna a Isiraeli chinali ichi:+
2 Amenewa anabwera pamodzi ndi Zerubabele,+ Yesuwa,*+ Nehemiya, Seraya, Reelaya, Moredikayi, Bilisani, Misipara, Bigivai, Rehumu ndi Bana. Chiwerengero cha amuna a Isiraeli chinali ichi:+