Ezara 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Alevi:+ Ana a Yesuwa, a mʼbanja la Kadimiyeli+ ochokera pakati pa ana a Hodaviya, 74.