Ezara 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuyambira nthawi imeneyo, anthu amʼdzikolo anayamba kufooketsa* anthu a ku Yuda komanso kuwagwetsa ulesi kuti asapitirize ntchito yomanga.+
4 Kuyambira nthawi imeneyo, anthu amʼdzikolo anayamba kufooketsa* anthu a ku Yuda komanso kuwagwetsa ulesi kuti asapitirize ntchito yomanga.+