Ezara 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mʼmasiku a Aritasasita mfumu ya Perisiya, Bisilamu, Mitiredati, Tabeeli ndi anzake ena onse analembera kalata mfumuyo. Kalatayo anaimasulira mʼChiaramu+ nʼkuilemba mʼzilembo za Chiaramu.* Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:7 Nsanja ya Olonda,1/15/1986, tsa. 7
7 Mʼmasiku a Aritasasita mfumu ya Perisiya, Bisilamu, Mitiredati, Tabeeli ndi anzake ena onse analembera kalata mfumuyo. Kalatayo anaimasulira mʼChiaramu+ nʼkuilemba mʼzilembo za Chiaramu.*