Ezara 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 * Rehumu mtsogoleri wa akuluakulu a boma ndi Simusai mlembi, analemba kalata yopita kwa mfumu Aritasasita yonena zoipa za anthu a ku Yerusalemu. Analemba kuti:
8 * Rehumu mtsogoleri wa akuluakulu a boma ndi Simusai mlembi, analemba kalata yopita kwa mfumu Aritasasita yonena zoipa za anthu a ku Yerusalemu. Analemba kuti: