Ezara 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (Inachokera kwa Rehumu mtsogoleri wa akuluakulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse monga oweruza ndi abwanamkubwa aangʼono, alembi ena, anthu a ku Ereke,+ Ababulo, anthu a ku Susa,+ kapena kuti Aelamu,+
9 (Inachokera kwa Rehumu mtsogoleri wa akuluakulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse monga oweruza ndi abwanamkubwa aangʼono, alembi ena, anthu a ku Ereke,+ Ababulo, anthu a ku Susa,+ kapena kuti Aelamu,+