Ezara 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 inu mfumu dziwani kuti Ayuda amene anachokera kwa inu nʼkubwera kuno afika ku Yerusalemu. Iwo akumanganso mzinda woukira ndiponso woipa uja. Akumanganso mpanda+ komanso kukonza maziko.
12 inu mfumu dziwani kuti Ayuda amene anachokera kwa inu nʼkubwera kuno afika ku Yerusalemu. Iwo akumanganso mzinda woukira ndiponso woipa uja. Akumanganso mpanda+ komanso kukonza maziko.