15 nʼcholinga choti mufufuze mʼbuku la mbiri ya makolo anu.+ Mukafufuza mʼbukulo mupeza kuti umenewu ndi mzinda woukira mafumu ndi zigawo za mayiko. Mumzinda umenewu mwakhala muli anthu oyambitsa kugalukira kuyambira kalekale. Nʼchifukwa chake mzindawu unawonongedwa.+