-
Ezara 4:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndiyeno mfumuyo inatumiza uthenga kwa Rehumu mtsogoleri wa akuluakulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse amene ankakhala ku Samariya ndiponso kwa ena onse omwe ankakhala kutsidya lina la Mtsinje. Uthengawo unali wakuti:
“Moni!
-