-
Ezara 4:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mawu amene analembedwa mʼkalata ya mfumu Aritasasita anawerengedwa pamaso pa Rehumu, Simusai mlembi ndi anzawo. Kenako iwo anapita msangamsanga kwa Ayuda ku Yerusalemu nʼkukawaletsa ntchitoyo mwankhondo.
-