Ezara 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa nthawi imeneyi mʼpamene ntchito yomanga nyumba ya Mulungu, imene inali ku Yerusalemu, inaima ndipo inaima choncho mpaka chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo mfumu ya Perisiya.+ Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:24 Nsanja ya Olonda,1/15/1986, tsa. 7
24 Pa nthawi imeneyi mʼpamene ntchito yomanga nyumba ya Mulungu, imene inali ku Yerusalemu, inaima ndipo inaima choncho mpaka chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo mfumu ya Perisiya.+