Ezara 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawi imeneyo Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,* Setara-bozenai ndi anzawo anabwera kwa Ayudawo nʼkuwafunsa kuti: “Kodi ndi ndani wakulamulani kuti mumange nyumbayi komanso kumaliza ntchitoyi?”* Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:3 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2017, tsa. 9
3 Pa nthawi imeneyo Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,* Setara-bozenai ndi anzawo anabwera kwa Ayudawo nʼkuwafunsa kuti: “Kodi ndi ndani wakulamulani kuti mumange nyumbayi komanso kumaliza ntchitoyi?”*