-
Ezara 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Inu mfumu dziwani kuti ife tinapita kuchigawo cha Yuda kunyumba ya Mulungu wamkulu. Kumeneko takapeza kuti nyumbayo akuimanga ndi miyala yochita kugubuduza ndiponso akuika matabwa mʼmakoma ake. Iwo akugwira ntchitoyo mwakhama ndipo ikuyenda bwino.
-