Ezara 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anatiyankha kuti: ‘Ndife atumiki a Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi. Tikumanganso nyumba imene inamangidwa zaka zambiri zapitazo, imene mfumu yaikulu ya Isiraeli inamanga nʼkuimaliza.+
11 Iwo anatiyankha kuti: ‘Ndife atumiki a Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi. Tikumanganso nyumba imene inamangidwa zaka zambiri zapitazo, imene mfumu yaikulu ya Isiraeli inamanga nʼkuimaliza.+