-
Ezara 6:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Pa nthawiyi mʼpamene mfumu Dariyo inaika lamulo loti afufuze mʼnyumba yosungiramo zinthu zakale, momwe ankasungamonso zinthu zamtengo wapatali zimene zinapititsidwa ku Babulo.
-