5 Ziwiya zagolide ndi zasiliva za mʼnyumba ya Mulungu, zimene Nebukadinezara anatenga mʼkachisi yemwe anali ku Yerusalemu nʼkuzipititsa ku Babulo,+ zibwezedwe kuti zikaikidwe kumalo ake, kukachisi amene ali ku Yerusalemu ndipo zikaikidwe mʼnyumba ya Mulungu.’+