Ezara 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano inu Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,* Setara-bozenai ndi anzanu ndiponso abwanamkubwa aangʼono amene ali kutsidya lina la Mtsinje,+ musapite kumeneko.
6 Tsopano inu Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,* Setara-bozenai ndi anzanu ndiponso abwanamkubwa aangʼono amene ali kutsidya lina la Mtsinje,+ musapite kumeneko.