-
Ezara 6:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Komanso muziwapatsa zinthu zomwe akufunikira monga ngʼombe zingʼonozingʼono zamphongo,+ nkhosa zamphongo+ ndi ana a nkhosa+ kuti azipereka nsembe yopsereza kwa Mulungu wakumwamba. Muziwapatsanso tirigu,+ mchere,+ vinyo+ ndi mafuta+ mogwirizana ndi zimene ansembe amene ali ku Yerusalemu anganene. Muziwapatsa zinthu zimenezi tsiku ndi tsiku
-