Ezara 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 kuti nthawi zonse azipereka nsembe zosangalatsa Mulungu wakumwamba ndiponso kuti azipempherera mfumu ndi ana ake kuti akhale ndi moyo wabwino.+
10 kuti nthawi zonse azipereka nsembe zosangalatsa Mulungu wakumwamba ndiponso kuti azipempherera mfumu ndi ana ake kuti akhale ndi moyo wabwino.+