Ezara 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Aisiraeli amene anabwera kuchokera ku ukapolo anadya nyamayo. Komanso aliyense amene anadzilekanitsa ku zonyansa za anthu a mitundu yamʼdzikolo nʼkubwera kwa iwo kuti alambire* Yehova Mulungu wa Isiraeli, anadya nawo.+ Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:21 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 191/15/1986, tsa. 29
21 Ndiyeno Aisiraeli amene anabwera kuchokera ku ukapolo anadya nyamayo. Komanso aliyense amene anadzilekanitsa ku zonyansa za anthu a mitundu yamʼdzikolo nʼkubwera kwa iwo kuti alambire* Yehova Mulungu wa Isiraeli, anadya nawo.+