Ezara 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zitachitika, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, Ezara*+ anabwera ku Yerusalemu kuchokera ku Babulo. Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+ Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:1 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 191/15/1986, ptsa. 7, 29
7 Zimenezi zitachitika, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, Ezara*+ anabwera ku Yerusalemu kuchokera ku Babulo. Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+