Ezara 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ahitubu anali mwana wa Amariya, Amariya anali mwana wa Azariya,+ Azariya anali mwana wa Merayoti,