Ezara 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Izi nʼzimene zinali mʼkalata imene Mfumu Aritasasita inapereka kwa wansembe Ezara wokopera Malemba,* katswiri pophunzira* malamulo a Yehova ndi malangizo amene anapereka kwa Aisiraeli: Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:11 Nsanja ya Olonda,1/15/1986, tsa. 29
11 Izi nʼzimene zinali mʼkalata imene Mfumu Aritasasita inapereka kwa wansembe Ezara wokopera Malemba,* katswiri pophunzira* malamulo a Yehova ndi malangizo amene anapereka kwa Aisiraeli: