Ezara 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 * “Kuchokera kwa Aritasasita,+ mfumu ya mafumu, kupita kwa wansembe Ezara, wokopera* Chilamulo cha Mulungu wakumwamba: Mtendere ukhale nawe. Tsopano
12 * “Kuchokera kwa Aritasasita,+ mfumu ya mafumu, kupita kwa wansembe Ezara, wokopera* Chilamulo cha Mulungu wakumwamba: Mtendere ukhale nawe. Tsopano