Ezara 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndalamazi ukagulire mwamsangamsanga ngʼombe zamphongo,+ nkhosa zamphongo,+ ana a nkhosa,+ limodzi ndi nsembe zake zambewu+ ndiponso nsembe zake zachakumwa.+ Zimenezi ukazipereke paguwa lansembe lapanyumba ya Mulungu wako, yomwe ili ku Yerusalemu.
17 Ndalamazi ukagulire mwamsangamsanga ngʼombe zamphongo,+ nkhosa zamphongo,+ ana a nkhosa,+ limodzi ndi nsembe zake zambewu+ ndiponso nsembe zake zachakumwa.+ Zimenezi ukazipereke paguwa lansembe lapanyumba ya Mulungu wako, yomwe ili ku Yerusalemu.