Ezara 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ziwiya zimene wapatsidwa kuti zikagwiritsidwe ntchito pa utumiki wapanyumba ya Mulungu wako, ukaziike pamaso pa Mulungu ku Yerusalemu.+
19 Ziwiya zimene wapatsidwa kuti zikagwiritsidwe ntchito pa utumiki wapanyumba ya Mulungu wako, ukaziike pamaso pa Mulungu ku Yerusalemu.+