Ezara 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zinthu zina zonse zofunika panyumba ya Mulungu wako zimene ukuyenera kupereka, ukazitenge kunyumba yosungiramo chuma cha mfumu.+
20 Zinthu zina zonse zofunika panyumba ya Mulungu wako zimene ukuyenera kupereka, ukazitenge kunyumba yosungiramo chuma cha mfumu.+